1 Akorinto 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero abale, sindinathe kulankhula nanu monga anthu auzimu,+ koma monga anthu oganiza ngati anthu a mādzikoli,* monga tiana+ mwa Khristu.
3 Chotero abale, sindinathe kulankhula nanu monga anthu auzimu,+ koma monga anthu oganiza ngati anthu a mādzikoli,* monga tiana+ mwa Khristu.