1 Akorinto 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kodi akukupangitsa kukhala wosiyana+ ndi ena ndani? Inde, uli ndi chiyani chimene sunachite kulandira?+ Ndiye ngati unachita kulandira zinthu zimenezo,+ n’chifukwa chiyani ukudzitama+ ngati kuti sunachite kulandira?
7 Kodi akukupangitsa kukhala wosiyana+ ndi ena ndani? Inde, uli ndi chiyani chimene sunachite kulandira?+ Ndiye ngati unachita kulandira zinthu zimenezo,+ n’chifukwa chiyani ukudzitama+ ngati kuti sunachite kulandira?