1 Akorinto 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ponyozedwa, timayankha mofatsa.+ Mpaka tsopano, takhala ngati zinyalala za dziko, nyansi za zinthu zonse.+
13 Ponyozedwa, timayankha mofatsa.+ Mpaka tsopano, takhala ngati zinyalala za dziko, nyansi za zinthu zonse.+