1 Akorinto 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti aliyense amene ali mwa Ambuye amene anaitanidwa ali kapolo ndi womasulidwa wa Ambuye,+ momwemonso amene anaitanidwa ali mfulu+ ndi kapolo+ wa Khristu. 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2144
22 Pakuti aliyense amene ali mwa Ambuye amene anaitanidwa ali kapolo ndi womasulidwa wa Ambuye,+ momwemonso amene anaitanidwa ali mfulu+ ndi kapolo+ wa Khristu.