1 Akorinto 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti ngati wina angaone iweyo wodziwa zinthuwe ukudya chakudya m’kachisi wa mafano, kodi chikumbumtima cha munthu wofooka uja sichidzamulimbikitsa kudya zakudya zoperekedwa kwa mafano?+
10 Pakuti ngati wina angaone iweyo wodziwa zinthuwe ukudya chakudya m’kachisi wa mafano, kodi chikumbumtima cha munthu wofooka uja sichidzamulimbikitsa kudya zakudya zoperekedwa kwa mafano?+