1 Akorinto 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano ndikukuyamikirani chifukwa chakuti mukundikumbukira m’zinthu zonse, ndipo mukusunga miyambo+ monga mmene ndinaiperekera kwa inu. 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:2 Nsanja ya Olonda,12/1/1995, ptsa. 3-412/1/1988, tsa. 7
2 Tsopano ndikukuyamikirani chifukwa chakuti mukundikumbukira m’zinthu zonse, ndipo mukusunga miyambo+ monga mmene ndinaiperekera kwa inu.