1 Akorinto 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngati mkazi savala kanthu kumutu, amete mpala, koma ngati zili zochititsa manyazi kuti mkazi amete kwambiri tsitsi lake kapena amete mpala,+ azivala chakumutu.+
6 Ngati mkazi savala kanthu kumutu, amete mpala, koma ngati zili zochititsa manyazi kuti mkazi amete kwambiri tsitsi lake kapena amete mpala,+ azivala chakumutu.+