1 Akorinto 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komabe, ngati alipo wina amene akuoneka kuti akutsutsa+ zimenezi pofuna chikhalidwe china,+ ifeyo, monganso mipingo ya Mulungu, tilibe chikhalidwe chinanso.
16 Komabe, ngati alipo wina amene akuoneka kuti akutsutsa+ zimenezi pofuna chikhalidwe china,+ ifeyo, monganso mipingo ya Mulungu, tilibe chikhalidwe chinanso.