2 Akorinto 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Popeza tikukumana ndi masautso ambiri chifukwa cha Khristu,+ tikutonthozedwanso kwambiri kudzera mwa Khristu.+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:5 Nsanja ya Olonda,11/1/1996, tsa. 14
5 Popeza tikukumana ndi masautso ambiri chifukwa cha Khristu,+ tikutonthozedwanso kwambiri kudzera mwa Khristu.+