2 Akorinto 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero chiyembekezo chathu mwa inu sichikugwedera, podziwa kuti mukukumana ndi masautso ofanana ndi amene ifeyo tikukumana nawo, inunso mudzatonthozedwa ngati ifeyo.+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:7 Nsanja ya Olonda,11/1/1996, ptsa. 12-13, 14-16
7 Chotero chiyembekezo chathu mwa inu sichikugwedera, podziwa kuti mukukumana ndi masautso ofanana ndi amene ifeyo tikukumana nawo, inunso mudzatonthozedwa ngati ifeyo.+