2 Akorinto 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho, popeza ndine wotsimikiza za zimenezi, ndinali ndi cholinga chofika kwa inu poyamba,+ kuti mudzakhale ndi mwayi wachiwiri+ wosangalala. 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:15 Nsanja ya Olonda,3/15/2014, ptsa. 30-31
15 Choncho, popeza ndine wotsimikiza za zimenezi, ndinali ndi cholinga chofika kwa inu poyamba,+ kuti mudzakhale ndi mwayi wachiwiri+ wosangalala.