2 Akorinto 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiponso malonjezo a Mulungu, kaya akhale ochuluka chotani,+ akhala Inde kudzera mwa iye.+ Choteronso kudzera mwa iye, “Ame”+ amanenedwa kwa Mulungu kuti Mulungu alandire ulemerero kudzera mwa ife. 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:20 Nsanja ya Olonda,3/15/2014, tsa. 3112/15/2008, tsa. 13
20 Ndiponso malonjezo a Mulungu, kaya akhale ochuluka chotani,+ akhala Inde kudzera mwa iye.+ Choteronso kudzera mwa iye, “Ame”+ amanenedwa kwa Mulungu kuti Mulungu alandire ulemerero kudzera mwa ife.