2 Akorinto 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mulungu akhale mboni+ pa moyo wanga kuti chifukwa chimene sindinabwererebe ku Korintoko n’chakuti sindinafune kuti ndidzawonjezere chisoni chanu.+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:23 Nsanja ya Olonda,10/15/2012, tsa. 29
23 Mulungu akhale mboni+ pa moyo wanga kuti chifukwa chimene sindinabwererebe ku Korintoko n’chakuti sindinafune kuti ndidzawonjezere chisoni chanu.+