15 Pakuti zonsezi zachitika chifukwa cha ubwino wanu.+ Ndiponso zachitika kuti kukoma mtima kwakukulu kumene kunawonjezeka kuchulukebe chifukwa cha anthu ambiri amene akupereka mapemphero oyamikira, zimene zikuchititsa kuti Mulungu alandire ulemerero.+