2 Akorinto 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndithudi, ngakhale kuti ndinakulemberani, sindinatero chifukwa cha wolakwayo+ kapena wolakwiridwayo ayi, koma kuti khama lanu lofuna kumvera mawu athu lionekere pamaso pa Mulungu.
12 Ndithudi, ngakhale kuti ndinakulemberani, sindinatero chifukwa cha wolakwayo+ kapena wolakwiridwayo ayi, koma kuti khama lanu lofuna kumvera mawu athu lionekere pamaso pa Mulungu.