2 Akorinto 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti mukudziwa kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye wathu Yesu Khristu, kuti ngakhale kuti iye anali wolemera, anakhala wosauka chifukwa cha inu,+ kuti inuyo mulemere+ kudzera m’kusauka kwake. 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:9 Nsanja ya Olonda,2/15/1992, ptsa. 16-171/15/1992, ptsa. 16-17
9 Pakuti mukudziwa kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye wathu Yesu Khristu, kuti ngakhale kuti iye anali wolemera, anakhala wosauka chifukwa cha inu,+ kuti inuyo mulemere+ kudzera m’kusauka kwake.