-
2 Akorinto 8:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Komanso pamodzi ndi iye, tikutumiza m’bale wina amene akutamandidwa m’mipingo yonse chifukwa cha zimene akuchita zokhudzana ndi uthenga wabwino.
-