2 Akorinto 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndithudi timasangalala nthawi zonse inu mukakhala amphamvu, pamene ife tili ofooka.+ Ndipo chimene tikupempherera+ n’chakuti musinthe zinthu zimene mukuyenera kusintha. 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:9 Nsanja ya Olonda,11/1/1990, ptsa. 29-31
9 Ndithudi timasangalala nthawi zonse inu mukakhala amphamvu, pamene ife tili ofooka.+ Ndipo chimene tikupempherera+ n’chakuti musinthe zinthu zimene mukuyenera kusintha.