Agalatiya 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndikukhulupirira+ kuti inu amene muli ogwirizana+ ndi Ambuye, simudzasintha maganizo, koma munthu amene amakuvutitsani,+ adzaweruzidwa+ kaya akhale ndani.
10 Ndikukhulupirira+ kuti inu amene muli ogwirizana+ ndi Ambuye, simudzasintha maganizo, koma munthu amene amakuvutitsani,+ adzaweruzidwa+ kaya akhale ndani.