Aefeso 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ndiponso kuti ndionetse anthu mmene chinsinsi chopatulikacho+ chikuyendetsedwera.+ Kuyambira kalekale, chinsinsi chimenechi chakhala chobisika mwa —Mulungu, amene analenga zinthu zonse.+
9 ndiponso kuti ndionetse anthu mmene chinsinsi chopatulikacho+ chikuyendetsedwera.+ Kuyambira kalekale, chinsinsi chimenechi chakhala chobisika mwa —Mulungu, amene analenga zinthu zonse.+