Aefeso 5:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Chinsinsi chopatulika+ chimenechi n’chachikulu. Tsopano ndikulankhula za Khristu ndi mpingo.+