-
Afilipi 2:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Choncho, ndikumutumiza mofulumira kwambiri, kuti inu mukamuona musangalale, ndiponso kuti chisoni changa chichepe.
-