Afilipi 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano kwa Mulungu wathu ndi Atate, kukhale ulemerero mpaka muyaya.+ Ame.