Akolose 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kudzera mwa iyeyo, inu simukusowa kalikonse. Iye ndiye mwini ulamuliro wonse ndi mphamvu zonse.+