Akolose 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muzilimbikira kupemphera.+ Mukhale maso pa nkhani ya kupemphera ndipo mukhale oyamikira.+