Akolose 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo kalatayi mukaiwerenga kwanuko, konzani zoti ikawerengedwenso+ ku mpingo wa Alaodikaya, ndiponso mukawerenge yochokera ku Laodikaya. Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:16 Nsanja ya Olonda,8/15/2008, tsa. 2811/15/1990, tsa. 26
16 Ndipo kalatayi mukaiwerenga kwanuko, konzani zoti ikawerengedwenso+ ku mpingo wa Alaodikaya, ndiponso mukawerenge yochokera ku Laodikaya.