1 Atesalonika 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Sitinali kungodzifunira ulemerero kwa anthu+ ayi, kaya kwa inu kapena kwa anthu ena. Sitinatero, ngakhale kuti monga atumwi a Khristu, tikanatha kupempha kuti mutilipirire+ zinthu zina kuti mutithandize.
6 Sitinali kungodzifunira ulemerero kwa anthu+ ayi, kaya kwa inu kapena kwa anthu ena. Sitinatero, ngakhale kuti monga atumwi a Khristu, tikanatha kupempha kuti mutilipirire+ zinthu zina kuti mutithandize.