1 Atesalonika 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho popeza timakukondani kwambiri,+ tinali okonzeka kukupatsani uthenga wabwino wa Mulungu. Ndipotu osati uthenga wokha ayi, komanso miyoyo+ yathu yeniyeniyo, chifukwa tinakukondani kwambiri.+ 1 Atesalonika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:8 Nsanja ya Olonda,11/15/2000, tsa. 2210/1/1986, tsa. 10
8 Choncho popeza timakukondani kwambiri,+ tinali okonzeka kukupatsani uthenga wabwino wa Mulungu. Ndipotu osati uthenga wokha ayi, komanso miyoyo+ yathu yeniyeniyo, chifukwa tinakukondani kwambiri.+