1 Atesalonika 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu ndinu mboni, Mulungunso ndi mboni, za mmene tinakhalira okhulupirika, olungama, ndi opanda chifukwa chotinenezera,+ kwa inu okhulupirira.
10 Inu ndinu mboni, Mulungunso ndi mboni, za mmene tinakhalira okhulupirika, olungama, ndi opanda chifukwa chotinenezera,+ kwa inu okhulupirira.