1 Atesalonika 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti inu abale munatsanzira mipingo ya Mulungu yogwirizana ndi Khristu Yesu imene ili ku Yudeya. Munatero chifukwa inunso munayamba kuvutitsidwa+ ndi anthu akwanu, ngati mmene iwonso akuvutitsidwira ndi Ayuda,
14 Pakuti inu abale munatsanzira mipingo ya Mulungu yogwirizana ndi Khristu Yesu imene ili ku Yudeya. Munatero chifukwa inunso munayamba kuvutitsidwa+ ndi anthu akwanu, ngati mmene iwonso akuvutitsidwira ndi Ayuda,