2 Timoteyo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pajatu onse ofuna kukhala ndi moyo wodzipereka kwa Mulungu mwa Khristu Yesu, nawonso adzazunzidwa.+ 2 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:12 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 59 Nsanja ya Olonda,8/15/2007, tsa. 14
12 Pajatu onse ofuna kukhala ndi moyo wodzipereka kwa Mulungu mwa Khristu Yesu, nawonso adzazunzidwa.+