-
2 Timoteyo 4:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Uchite chilichonse chotheka kuti ufike kuno nyengo yachisanu isanayambe.
Ebulo, Pude, Lino ndiponso Kalaudiya ndi abale onse, akupereka moni.
-