Aheberi 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Uthenga wabwino unalengezedwa kwa ife,+ monga mmenenso unalengezedwera kwa makolo athu.+ Koma mawu amene iwo anamva sanapindule nawo,+ chifukwa sanakhale ndi chikhulupiriro+ ngati cha amene anamvera mawuwo.+
2 Uthenga wabwino unalengezedwa kwa ife,+ monga mmenenso unalengezedwera kwa makolo athu.+ Koma mawu amene iwo anamva sanapindule nawo,+ chifukwa sanakhale ndi chikhulupiriro+ ngati cha amene anamvera mawuwo.+