Aheberi 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Komanso, wansembe aliyense amaima pamalo ake+ kuti achite ntchito yotumikira ena ndi kupereka nsembe zimodzimodzizo mobwerezabwereza,+ popeza zimenezi sizingachotseretu machimo.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:11 Nsanja ya Olonda,11/15/2000, tsa. 11
11 Komanso, wansembe aliyense amaima pamalo ake+ kuti achite ntchito yotumikira ena ndi kupereka nsembe zimodzimodzizo mobwerezabwereza,+ popeza zimenezi sizingachotseretu machimo.+