Aheberi 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwa chikhulupiriro, Sara+ nayenso analandira mphamvu yokhala ndi pakati* ngakhale kuti anali atapitirira zaka zobereka,+ chifukwa anaona kuti wolonjezayo ndi wokhulupirika.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:11 Nsanja ya Olonda,5/15/2015, tsa. 217/15/1993, tsa. 171/15/1987, tsa. 12
11 Mwa chikhulupiriro, Sara+ nayenso analandira mphamvu yokhala ndi pakati* ngakhale kuti anali atapitirira zaka zobereka,+ chifukwa anaona kuti wolonjezayo ndi wokhulupirika.+