Aheberi 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mwa chikhulupiriro, Yosefe atayandikira mapeto a moyo wake, anatchula za kusamuka+ kwa ana a Isiraeli, ndipo anapereka lamulo lokhudza mafupa ake.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:22 Nsanja ya Olonda,6/1/2007, tsa. 28
22 Mwa chikhulupiriro, Yosefe atayandikira mapeto a moyo wake, anatchula za kusamuka+ kwa ana a Isiraeli, ndipo anapereka lamulo lokhudza mafupa ake.+