Aheberi 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Nanga ndinenenso chiyani pamenepa? Nthawi indichepera kuti ndipitirize kufotokoza za Gidiyoni,+ Baraki,+ Samisoni,+ Yefita,+ Davide,+ komanso Samueli+ ndi aneneri enanso.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:32 Tsanzirani, ptsa. 70-71 Nsanja ya Olonda,1/1/2011, ptsa. 25-261/15/1987, ptsa. 16-17
32 Nanga ndinenenso chiyani pamenepa? Nthawi indichepera kuti ndipitirize kufotokoza za Gidiyoni,+ Baraki,+ Samisoni,+ Yefita,+ Davide,+ komanso Samueli+ ndi aneneri enanso.+