Aheberi 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pochita zimenezo, muonetsetse kuti wina asalandidwe kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu,+ komanso kuti pakati panu pasatuluke muzu wapoizoni+ woyambitsa mavuto, ndi kuti ambiri asaipitsidwe nawo.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:15 Nsanja ya Olonda,10/15/2008, tsa. 3211/1/2006, tsa. 2612/15/1989, tsa. 14
15 Pochita zimenezo, muonetsetse kuti wina asalandidwe kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu,+ komanso kuti pakati panu pasatuluke muzu wapoizoni+ woyambitsa mavuto, ndi kuti ambiri asaipitsidwe nawo.+