Yakobo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tamverani abale anga okondedwa. Mulungu anasankha anthu amene ali osauka+ m’dzikoli kuti akhale olemera+ m’chikhulupiriro ndi olandira cholowa cha ufumu umene anaulonjeza kwa omukonda,+ sanatero kodi? Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:5 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, tsa. 14
5 Tamverani abale anga okondedwa. Mulungu anasankha anthu amene ali osauka+ m’dzikoli kuti akhale olemera+ m’chikhulupiriro ndi olandira cholowa cha ufumu umene anaulonjeza kwa omukonda,+ sanatero kodi?