Yakobo 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Umakhulupirira kuti kuli Mulungu mmodzi, si choncho?+ Ukuchita bwino. Koma ziwanda nazonso zimakhulupirira ndipo zimanjenjemera.+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:19 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2016, ptsa. 28-29 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, tsa. 15
19 Umakhulupirira kuti kuli Mulungu mmodzi, si choncho?+ Ukuchita bwino. Koma ziwanda nazonso zimakhulupirira ndipo zimanjenjemera.+