Yakobo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Lilimenso ndi moto.+ Mwa ziwalo zathu zonse, lilime ndilo lili lodzaza ndi zosalungama chifukwa limadetsa thupi lonse.+ Lili ndi moto wa Gehena* ndipo limayatsa moyo wonse wa munthu. Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:6 Nsanja ya Olonda,12/15/2015, ptsa. 18-198/15/2012, ptsa. 20-2111/15/1997, ptsa. 16-17
6 Lilimenso ndi moto.+ Mwa ziwalo zathu zonse, lilime ndilo lili lodzaza ndi zosalungama chifukwa limadetsa thupi lonse.+ Lili ndi moto wa Gehena* ndipo limayatsa moyo wonse wa munthu.