Yakobo 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakamwa pamodzimodzipo pamatuluka mawu otamanda ndi otemberera. N’kosayenera abale anga kuti zinthu zimenezi zipitirire kuchitika motere.+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:10 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, ptsa. 17-187/15/1993, tsa. 21
10 Pakamwa pamodzimodzipo pamatuluka mawu otamanda ndi otemberera. N’kosayenera abale anga kuti zinthu zimenezi zipitirire kuchitika motere.+