Yakobo 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mumalakalaka, koma simukhala nazo. Mumapha anthu+ ndiponso mumasirira mwansanje,+ koma simupeza kanthu. Mumakangana+ ndiponso mumachita nkhondo. Simukhala ndi kanthu chifukwa simupempha. Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:2 Nsanja ya Olonda,9/1/1998, tsa. 1211/15/1997, tsa. 199/15/1995, tsa. 4
2 Mumalakalaka, koma simukhala nazo. Mumapha anthu+ ndiponso mumasirira mwansanje,+ koma simupeza kanthu. Mumakangana+ ndiponso mumachita nkhondo. Simukhala ndi kanthu chifukwa simupempha.