1 Petulo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ngati anthu akukunyozani chifukwa cha dzina la Khristu,+ ndinu odala+ chifukwa zikusonyeza kuti mzimu waulemerero, umene ndi mzimu wa Mulungu, wakhazikika pa inu.+ 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:14 Nsanja ya Olonda,7/15/2014, tsa. 32
14 Ngati anthu akukunyozani chifukwa cha dzina la Khristu,+ ndinu odala+ chifukwa zikusonyeza kuti mzimu waulemerero, umene ndi mzimu wa Mulungu, wakhazikika pa inu.+