1 Petulo 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ngati akuvutika+ chifukwa chokhala Mkhristu, asachite manyazi,+ koma apitirize kulemekeza Mulungu m’dzina la Khristuyo.
16 Koma ngati akuvutika+ chifukwa chokhala Mkhristu, asachite manyazi,+ koma apitirize kulemekeza Mulungu m’dzina la Khristuyo.