1 Petulo 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Patsanani moni popsompsonana mwa chikondi chaubale.+ Nonse amene muli ogwirizana ndi Khristu, mtendere ukhale nanu.+ 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:14 Nsanja ya Olonda,10/15/1993, tsa. 15
14 Patsanani moni popsompsonana mwa chikondi chaubale.+ Nonse amene muli ogwirizana ndi Khristu, mtendere ukhale nanu.+