1 Yohane 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Tikukulemberani za iye amene analiko kuyambira pa chiyambi,+ amene amabweretsa mawu opatsa moyo,+ amene tamumva+ ndiponso kumuona ndi maso athu,+ amene tamuyang’anitsitsa+ mwachidwi ndi kumukhudza ndi manja athu.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:1 Nsanja ya Olonda,1/15/1987, tsa. 26
1 Tikukulemberani za iye amene analiko kuyambira pa chiyambi,+ amene amabweretsa mawu opatsa moyo,+ amene tamumva+ ndiponso kumuona ndi maso athu,+ amene tamuyang’anitsitsa+ mwachidwi ndi kumukhudza ndi manja athu.+