1 Yohane 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komabe, ndikukulemberani lamulo latsopano limene Yesu analitsatira, limenenso inuyo mukulitsatira, chifukwa chakuti mdima+ ukupita ndipo kuwala kwenikweni+ kwayamba kale kuunika. 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:8 Nsanja ya Olonda,12/15/2008, tsa. 271/15/1987, tsa. 28
8 Komabe, ndikukulemberani lamulo latsopano limene Yesu analitsatira, limenenso inuyo mukulitsatira, chifukwa chakuti mdima+ ukupita ndipo kuwala kwenikweni+ kwayamba kale kuunika.