1 Yohane 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tsopano inu ana anga okondedwa,+ khalanibe ogwirizana+ naye, kuti akadzaonetsedwa,+ tidzakhale ndi ufulu wa kulankhula.+ Kutinso tisadzachititsidwe manyazi ndi kuchotsedwa kwa iye pa nthawi ya kukhalapo*+ kwake. 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:28 Nsanja ya Olonda,1/15/1987, ptsa. 15-30
28 Tsopano inu ana anga okondedwa,+ khalanibe ogwirizana+ naye, kuti akadzaonetsedwa,+ tidzakhale ndi ufulu wa kulankhula.+ Kutinso tisadzachititsidwe manyazi ndi kuchotsedwa kwa iye pa nthawi ya kukhalapo*+ kwake.