Yuda 13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ali ngatinso mafunde oopsa a panyanja otulutsa thovu la zinthu zoyenera kuwachititsa manyazi,+ ndiponso nyenyezi zosochera, zimene azisungira mdima wandiweyani wosatha.+
13 Ali ngatinso mafunde oopsa a panyanja otulutsa thovu la zinthu zoyenera kuwachititsa manyazi,+ ndiponso nyenyezi zosochera, zimene azisungira mdima wandiweyani wosatha.+